Out Of My League

Out Of My League

Driemo Mw

Альбом: Mzaliwa
Длительность: 3:28
Год: 2023
Скачать MP3

Текст песни

It's Driemo
Mmmh
I say beauty yofunika medal
Timaso tokoka attention
Akamayenda ngati sanachimwepo
Polenga iwe ankaona angelo
M'maso mwanga ndamunveka vero
Koma olo dzina langa sanalimvepo
Zoti amandidziwa sindinganenepo
Awa ndi makina machine amphepo
Uyu ndi ndi mankhwala ozunguza bongo
Ona mpaka shasha wapinda mabondo
Kaya ikhala nkhondo tisenza mikondo
Kaya sandimvera tikaona konko ooh
Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa
Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa
This girl is out of my league
She's out of my league
This girl is out of my league
She's out of my league yah
Ali champions ndili mu super league
Ndili mu disco iye super gigi
Mu bus yake sindingapezemo seat
Ndili panja sitingachite link
Call me a soldier ndili pa mission
Never give up ndili ndi reason
Zikangovuta nditenga commission
Koma for now mayiwa ndi mission
Uyu ndi ndi mankhwala ozunguza bongo
Ona mpaka shasha wapinda mabondo
Kaya ikhala nkhondo tisenza mikondo
Kaya sandimvera tikaona konko ooh
Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa
Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa
This girl is out of my league
She's out of my league
This girl is out of my league
She's out of my league yah
To be honest zosiyana nzambiri
Zolekana nzambiri
Bwanji ndizisiye ndingaononge mbiri
Ndazipatsa malire
To be honest zosiyana nzambiri
Zolekana nzambiri
Bwanji ndizisiye ndingaononge mbiri
Ndazipatsa malire
Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa
Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa
This girl is out of my league
She's out of my league
This girl is out of my league
She's out of my league yah
Sangandimve olo ndita, olo ndita—kuwa
Sangayime olo ndita, olo ndita—kuwa
This girl is out of my league
She's out of my league
This girl is out of my league
She's out of my league yah