Musanagone
Lawi
Mulibe mtima wachikondi (amayi inu) Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu) Ndichiyani mukufuna (amayi inu) Kuti musangalale (kuti mama inu) Chikhala wena mukanayamika Achepelenji amuna a chikondi Akazi anzanu akulila mama Muli ndi tsoka losasimbika wawa Mukanjoyanjoya akazi wanga muzandipeza Nkhani zomwe ndikumazimva zikundiliza Ndinakutenga kumudzi uli ofatsa Unali mkazi wa ulemu kodi watani? Ine ndayesetsa kuonetsa chikondi changa Ndinali munthu ovuta ndinasintha ine Ku m'mawa ndikakusiya kuntchito kwanu Ndamva kuti ukumachoka ndi amuna ena Mulibe mtima wachikondi (amayi inu) Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu) Ndichiyani mukufuna? (amayi inu) Kuti musangalale (kodi mama inu) Chikhala wena mukanayamika Achepelenji amuna a chikondi Akazi anzanu akulila mama Muli ndi tsoka losasimbika wawa Zimamvetsa inu chisoni masiku ano Akazi atayilila mokhumudwitsa Amakudyetsa mankhwala ati upuse Chilichonse chomwe anene udzingolola Helele aha Ati kandisiye ku casino iwe kulola Akakumana ndi zibwenzi iwe ukugona Bambo wabwinobwino wazalezeka Kuthandiza akwawo onse anamuletsa Adamuletsa Adamuletsa Mulibe mtima wachikondi (amayi inu) Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu) Ndichiyani mukufuna? (amayi inu) Kuti musangalale (kodi mama inu) Chikhala wena mukanayamika Achepelenji amuna a chikondi Akazi anzanu akulila mama Muli ndi tsoka losasimbika wawa Helele ey hu yeah lemme go again (Three, two, one) Mulibe mtima wachikondi (amayi inu) Ndikapita ndi edzi (ndi amayi inu) Ndichiyani mukufuna (amayi inu) Kuti musangalale (kodi mama inu) Chikhala wena mukanayamika Achepelenji amuna a chikondi Akazi anzanu akulila mama Muli ndi tsoka losasimbika wawa