Musanagone
Lawi
Mmmh mami oh oh oh Baby oh Baby come back Oh ooh whoa Kodi dzulo timabwela kunja kukada Kodi komwe muliko Mukumakwanitsa kudya? Nanga ukumatha bwanji Kupita ku ntchito Ndafuna udziwe, ine sizikuyenda Kuchokera tsiku lomwe iwe udachoka Panyumba padasintha Lero ndine mulendo Bed kugula ndekha sindikwanitsa I want you to know My lucky pends on you Ndayamba ndi kale Kuyitana osabwera Mkazi wanga uliko? Tandiyankha ine ndidziwe Kuyang'anira kunjira Kuti mwina ndingakuone Mkazi wanga uliko? Tabwerera unandi-iwe Bwerera, bwerera iwe Bwerera, bwerera iwe Bwerera, bwerera iwe Bwerera, bwerera iwe Ndimkangoti sukachedwa ukabwerera Poganiza zabwino udasiya kumbuyo Ndimkangoti ukatuwa kapena kuguga Udzandigwadira, udzandichondelera Kodi ndi mwamuna uti wakuyiwalitsa ineyo Zukumandiwawa ukunjoya kopanda ine Akumandiuza anzanga anakuona Ukusangalala, moyo wako wasuntha Ndayamba ndi kale Kuyitana osabwera Mkazi wanga uliko? Tandiyankha ine ndidziwe Kuyang'anira kunjira Kuti mwina ndingakuone Mkazi wanga uliko? Tabwerera unandi-iwe Bwerera, bwerera iwe Bwerera, bwerera iwe Bwerera, bwerera iwe Bwerera, bwerera iwe Ndayamba ndi kale Kuyitana osabwera Mkazi wanga uliko? Tandiyankha ine ndidziwe Kuyang'anira kunjira Kuti mwina ndingakuone Mkazi wanga uliko? Tabwerera unandi-iwe Ndasintha ine, bwerera Sintha ine, bwerera iwe Ndalakwa ine, bwerera Bwerera iwe, bwerera iwe Bwerera iwe, bwerera iwe Bwerera iwe, bwerera iwe