Sangandilengere
Lawi
(Sley...) (D-D-D-D-D-D-Dj Sley) Heeeh, heeeh! Munthu wobadwa mwa mkazi ali choncho Lero aseke, mawa akukwiyire Akulandile, pomwepo akuwingitse Nsadalire, mtsamire kwa Jehovah It is better, walk with you Jesus It is safe, dwelling your pains Insecure, leaving your house Human beings have let me down Pamene ndimkasauka, anali kukondwa nane Akamanena za chuma chawo, ine nzichemelera Koma lero ndamuziwa, mwini wa chuma chapansi Sindizayenda ndi munthu Nzayenda ndi Yesuyo Nkokoma kuyenda ndi Ambuye Nkwabwino kukhala ndi Yesu Nkozuna kuyimbila Chauta Nkwabwino kukhala m'nyumba yake Nkokoma kuyenda ndi Ambuye Nkwabwino kukhala ndi Yesu Dziko lapansi lafika popweteka Chilungamo chasanduka tchimo Anthu akupha, achita kunyadila Awo akuba, achita kubonisa Tibisale nkhwapa mwanu Mbuye I want to walk under your shadow Ndifuna kuyimba, ndipate nzimu oyera I want to live under your influence Pamene ndimkasauka (aaa), anali kukondwa nane (aaa-aaa-aaa) Akamanena za chuma chawo (aaa), ine nzichemelera Koma lero ndamuziwa (aaa), mwini wa chuma chapansi (aaa-aaa-aaa) Sindizayenda ndi munthu Nzayenda ndi Yesuyo Nkokoma kuyenda ndi Ambuye Nkwabwino kukhala ndi Yesu Nkozuna kuyimbila Chauta Nkwabwino kukhala m'nyumba yake Nkokoma kuyenda ndi Ambuye Nkwabwino kukhala ndi Yesu Chimpinduliranji kwa munthu wapadziko Kupata zonse, kutaya moyo wake Poti zapadziko sizikwanira The more you have, the more you want to get Solomon (heh-heh) adati ndizachabe (chabe) Analinga (heh-heh) atakhala nazo (nazo) Anali ndi zonse zofuna moyo wake Koma ludzu wothetsa ndi Ambuye, yeah! Nkokoma kuyenda ndi Ambuye (Aaah nkwabwino) Nkwabwino kukhala ndi Yesu (Kuzuna, kuzuna, kuzuna mama) Nkozuna kuyimbila Chauta (eeh, he-he-he-he-he-he-heh) Nkwabwino kukhala m'nyumba yake (mkokomaaa!) Nkokoma kuyenda ndi Ambuye (mkozuna, zuna) Nkwabwino kukhala ndi Yesu (Nkokoma, Nkokoma) nkokoma kuyenda ndi Yesu Nko-nkoko-nkokoma, Oh! Nkwabwino kukhala ndi Yesu Nzofunika kukhala naye Nkozuna kuyimbila Chauta (moyo wanga mama, weh) Nkwabwino kukhala m'nyumba yake (ay, yeah-yeah-yeah ay, yoh-oh!) Nkokoma kuyenda ndi Yesu (nkoko, kuyenda ndi Yesuyo) Nkwabwino kukhala ndi Yesu (whoa Yesuyo) Oh, oh-oh whoa Nkokoma mamane weh (ooh) Nkokoma ma-ma-ma-ma-ma-ma (weh oh-whoa)