Akazi Ndi Maluwa
Marco Sadik
4:46Ngati chikondi m'mati chokoma Nanga ine bwanji kuwawa oh Bwenzi langa linali lokonda Mwalinamiza lelo lapita Kani ntimawanu ngoyipa inu Mulingati njoka mu udzu Ndazindikila yemwe amakupha Ndiodya naye mbale imodzi Chilichonse ndingapange mungonyoza Kulikonse mungapite mungolonda Anthu antundu wanji inu abodza Mutileke mutisiye Takondana basi Takondana basi Linda bwelela tizamange banja Chonde pilila tizasungane Chikondi ndi anthu awili enawa mabodza Wachitatu bwenzi langa osokoneza Amamasula amakaniza usamumvele Ngati uli undeta wakukwana Iwe tangoleka nsanje yako Ungotaya nthawi yako pa chabe Yesetsa kufuna uzapeza Ngati ukumakala kusowa chochita Paliponse ungayende ungobwebweta Chita manyazi ndipatse danga Uyu ndi wanga okondendwa Chilichonse ndingapange mungonyoza Kulikonse mungapite mungolonda Anthu antundu wanji inu abodza Mutileke mutisiye Takondana basi (oh no) Takondana basi Linda bwelela tizamange banja Chonde pilila tizasungane Chikondi ndi anthu awili enawa mabodza Wachitatu bwenzi langa ndiosokoneza Amamasula amakaniza usamumvele Pamene bwenzi lapita inu chimwemwe kusaya Kusangala kuti ine pamudzi ndikhale ndekha Komabe ndimuyitana iye abwelela Linda (iwe Linda bwelela iwe) Linda (iwe Linda bwelela iwe) Linda (iwe Linda bwelela iwe) Linda (chonde nkazi wanga) Linda bwelela tizamange banja Chonde pilila tizasungane Chikondi ndi anthu awili enawa mabodza Wachitatu bwenzi langa ndiosokoneza Amamasula amakaniza usamumvele Ndatopa nawo mabodza Dona yanga iyo Isiyeni yokha Nanenso Ndisiyeni ndekha Linda (iwe Linda bwelela iwe) Linda (iwe Linda bwelela iwe) Chikondi ndi anthu awili Chikondi ndi anthu awili Chikondi ndi anthu awili