Wanga
Taimon Tipa
3:51Taimon Ooh oooh ooh ooh! Ukamalimbikira Ulendo Sungathere panjira Ukudutsa muzopinga Tsiku lina utulukira Munthu ukamafika poiphula Umakhala wakhaula Achuluka okudelera Ena okukhomelera Mtima wako watopa Thupi lako lafooka Pena ngati ungozisiya Koma tiye Ndi ambiri okudalila Ndipo akuchulukira Ukazisiya adandaula iwe tiye Inde zambiri zakanika Aaah eeh siwe wekha Ifeso takanika aaah Eeh siwe wekha koma Ndife akulu akulu Zosatheka kumangolira Koma nafe tikudutsa Momwemo aah eeh siwe wekha Timadziwa mwanawe ndiwe Olimbikira koma tilibe Nthawi yokuombera m'manja Ena sakondwera kukuona Ukupita amatchinga njira Kuti usapeze podutsa eeeh Amangokhumba atakhala Yaweh ayimitse zako Zisayende dziko lonseli Adzisangalala okha Koma osamadzilembera Malile moyo uno ndi Vala zilimbe okhulupilira Tonse tidzidikira Mtima wako watopa Thupi lako lafooka Pena ngati ungozisiya Koma tiye ndi ambiri Okudalira ndipo akuchulukira Ukazisiya adandaula iwe tiye Inde zambiri zakanika Aaah eeh siwe wekha ifeso Takanika aah eeh siwe Wekha koma ndife akulu Akulu zosatheka kumangolila Koma nafe tikudutsa Momwemo aaah eeh siwe wekha Inde zambiri Zakanika Aah eeeh siwe wekha ifeso Takanika aah eeh siwe Wekha koma ndife akuluakulu Zosatheka kumangolira koma Name tudutsa momwemo Aah eeh siwe wekha