Notice: file_put_contents(): Write of 669 bytes failed with errno=28 No space left on device in /www/wwwroot/muzbon.net/system/url_helper.php on line 265
Billy Kaunda - Mtundu Wanga Ndisiye | Скачать MP3 бесплатно
Mtundu Wanga Ndisiye

Mtundu Wanga Ndisiye

Billy Kaunda

Длительность: 5:55
Год: 2014
Скачать MP3

Текст песни

Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

Mayo ndakulakwiranji iwe?
Mayo bwenzi lokondeka iwe
Mayo mtima ukuwawa bwanji iwe?
Mayo ndiyankhe tsopanoli iwe
Mtundu wanga, mtundu wanga iwe
Ndakulakwitra chani iwe?
Kuti mpakana undiphe iwe
Panalibe chilango china kodi iwe?
Chomwe ukanandipatsa ine

Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

Kodi ndine woyamba iwe?
Kuti ndikulakwire iwe
Sindinayembekezele iwe
Kuti mpaka ungandiphe iwe
Ndisanakaweluzidwe ine

Mayo wandipha ngati njoka ine
Mayo kodi umapemphera iwe?
Mayo kuyesa kufuula ine
Mayo osamva chisoni iwe
Pomwe umkandigwira iwe
Sindinafune kuthawa ine
Poti ndinali kudziwa ine
Kuti ndiwe mtundu wanga iwe
Tikakambirana zizatha iwe
Mayo kundimenya njira yonse iwe
Mayo pomangidwa mikono ine
Mayo tunthu wanga ndisiye iwe
Mayo ndafa imfa ya njoka ine

.Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah

.Whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah
Whoa, whoa, whoa, whoa, whoa, yeah yah